1 Samueli 31:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Nthawi yomweyo, amuna olimba mtima ananyamuka ndi kuyenda usiku wonse kukachotsa mtembo wa Sauli ndi mitembo ya ana ake pakhoma la ku Beti-sani. Kenako anabwerera ku Yabesi ndi kutentha mitemboyo kumeneko.+
12 Nthawi yomweyo, amuna olimba mtima ananyamuka ndi kuyenda usiku wonse kukachotsa mtembo wa Sauli ndi mitembo ya ana ake pakhoma la ku Beti-sani. Kenako anabwerera ku Yabesi ndi kutentha mitemboyo kumeneko.+