-
Amosi 6:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Ndipo m’bale wa bambo ake a mwamuna mmodzi mwa amuna ophedwawo adzawatulutsa ndi kuwatentha mmodzi ndi mmodzi kuti atulutse mafupa onse m’nyumbamo.+ Ndiyeno adzafunsa aliyense amene ali m’chipinda chamkatikati kuti, ‘Kodi muli anthu enanso mmenemo?’ Pamenepo amene ali m’chipindayo adzayankha kuti, ‘Mulibe!’ Kenako adzamuuza kuti, ‘Khala chete! Pakuti ino si nthawi yotchula dzina la Yehova.’”+
-