2 Mafumu 6:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Elisa ali mkati molankhula nawo, mthenga uja anafika, ndipo mfumu inati: “Tsokali lachokera kwa Yehova.+ Kodi pali chifukwa choti ndipitirizire kuyembekezera Yehova?”+
33 Elisa ali mkati molankhula nawo, mthenga uja anafika, ndipo mfumu inati: “Tsokali lachokera kwa Yehova.+ Kodi pali chifukwa choti ndipitirizire kuyembekezera Yehova?”+