1 Samueli 17:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mtengo wa mkondo wake unali waukulu ngati mtanda wa owomba nsalu,+ ndipo mutu wachitsulo wa mkondowo unali wolemera masekeli 600. Munthu womunyamulira chishango chake chachikulu anali kuyenda patsogolo pake.
7 Mtengo wa mkondo wake unali waukulu ngati mtanda wa owomba nsalu,+ ndipo mutu wachitsulo wa mkondowo unali wolemera masekeli 600. Munthu womunyamulira chishango chake chachikulu anali kuyenda patsogolo pake.