Deuteronomo 8:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Samalani kuti musaiwale+ Yehova Mulungu wanu ndi kusasunga malamulo, zigamulo ndi mfundo zake zimene ndikukupatsani lero.+ Salimo 18:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Zigamulo zake zonse zili pamaso panga,+Ndipo malamulo ake sindidzawataya.+
11 Samalani kuti musaiwale+ Yehova Mulungu wanu ndi kusasunga malamulo, zigamulo ndi mfundo zake zimene ndikukupatsani lero.+