Yobu 34:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Kuti achititse kulira kwa wonyozeka kupita kwa iye.Choncho iye amamva kulira kwa osautsika.+ Zefaniya 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mwa iwe ndidzasiyamo anthu ena, odzichepetsa ndi ofatsa,+ ndipo amenewa adzapeza chitetezo m’dzina la Yehova.+
12 Mwa iwe ndidzasiyamo anthu ena, odzichepetsa ndi ofatsa,+ ndipo amenewa adzapeza chitetezo m’dzina la Yehova.+