1 Mbiri 11:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ngakhale kuti anali wolemekezeka kuposa amuna 30 aja, iye sanafikepo pa amuna atatu oyamba aja.+ Komabe Davide anamuika kukhala mtsogoleri wa asilikali omulondera.+
25 Ngakhale kuti anali wolemekezeka kuposa amuna 30 aja, iye sanafikepo pa amuna atatu oyamba aja.+ Komabe Davide anamuika kukhala mtsogoleri wa asilikali omulondera.+