Oweruza 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndipo anamuika m’manda ku Timinati-heresi,*+ m’dera limene analandira monga cholowa chake, m’dera lamapiri la Efuraimu, kumpoto kwa phiri la Gaasi.+ 1 Mbiri 11:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Hurai wa kuzigwa* za Gaasi,+ Abiyeli Muaraba,
9 Ndipo anamuika m’manda ku Timinati-heresi,*+ m’dera limene analandira monga cholowa chake, m’dera lamapiri la Efuraimu, kumpoto kwa phiri la Gaasi.+