Oweruza 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndipo anamuika mʼmanda ku Timinati-heresi,+ mʼdera limene analandira monga cholowa chake, mʼdera lamapiri la Efuraimu, kumpoto kwa phiri la Gaasi.+
9 Ndipo anamuika mʼmanda ku Timinati-heresi,+ mʼdera limene analandira monga cholowa chake, mʼdera lamapiri la Efuraimu, kumpoto kwa phiri la Gaasi.+