Oweruza 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndipo anamuika m’manda ku Timinati-heresi,*+ m’dera limene analandira monga cholowa chake, m’dera lamapiri la Efuraimu, kumpoto kwa phiri la Gaasi.+
9 Ndipo anamuika m’manda ku Timinati-heresi,*+ m’dera limene analandira monga cholowa chake, m’dera lamapiri la Efuraimu, kumpoto kwa phiri la Gaasi.+