1 Mbiri 21:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Tsopano Satana anayamba kulimbana ndi Isiraeli polimbikitsa+ Davide kuti awerenge Aisiraeli. 1 Mbiri 27:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Davide sanawerenge amuna amene anali ndi zaka 20 kutsika m’munsi, chifukwa Yehova analonjeza kuti adzachulukitsa Aisiraeli ngati nyenyezi zakumwamba.+
23 Davide sanawerenge amuna amene anali ndi zaka 20 kutsika m’munsi, chifukwa Yehova analonjeza kuti adzachulukitsa Aisiraeli ngati nyenyezi zakumwamba.+