Yoswa 19:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Malirewo anakhota n’kubwerera ku Rama, mpaka kukafika kumzinda wa Turo+ wokhala ndi mpanda wolimba kwambiri. Kenako anakhotanso n’kubwerera ku Hosa n’kukathera kunyanja, m’chigawo cha Akizibu.+
29 Malirewo anakhota n’kubwerera ku Rama, mpaka kukafika kumzinda wa Turo+ wokhala ndi mpanda wolimba kwambiri. Kenako anakhotanso n’kubwerera ku Hosa n’kukathera kunyanja, m’chigawo cha Akizibu.+