Yoswa 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma amuna achiisiraeli anayankha Ahiviwo+ kuti: “Mwinamwake mumakhala pafupi chakonkuno. Ndiye tingachite nanu bwanji pangano?”+ Yoswa 11:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Panalibe mzinda winanso umene unapangana za mtendere ndi ana a Isiraeli kupatulapo Ahivi+ okhala mumzinda wa Gibeoni.+ Ana a Isiraeli analanda mizinda ina yonse mwankhondo.+
7 Koma amuna achiisiraeli anayankha Ahiviwo+ kuti: “Mwinamwake mumakhala pafupi chakonkuno. Ndiye tingachite nanu bwanji pangano?”+
19 Panalibe mzinda winanso umene unapangana za mtendere ndi ana a Isiraeli kupatulapo Ahivi+ okhala mumzinda wa Gibeoni.+ Ana a Isiraeli analanda mizinda ina yonse mwankhondo.+