Rute 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Atamva zimenezo anagwada n’kuwerama mpaka nkhope yake pansi,+ n’kunena kuti: “Zatheka bwanji kuti mundiganizire ndi kundikomera mtima chotere, ine wokhala mlendo?”+ 2 Samueli 9:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mefiboseti atamva zimenezi anawerama mpaka nkhope yake pansi ndipo anati: “Kodi ine mtumiki wanu ndine ndani kuti mukumbukire galu wakufa+ ngati ine?”
10 Atamva zimenezo anagwada n’kuwerama mpaka nkhope yake pansi,+ n’kunena kuti: “Zatheka bwanji kuti mundiganizire ndi kundikomera mtima chotere, ine wokhala mlendo?”+
8 Mefiboseti atamva zimenezi anawerama mpaka nkhope yake pansi ndipo anati: “Kodi ine mtumiki wanu ndine ndani kuti mukumbukire galu wakufa+ ngati ine?”