Levitiko 21:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Munthu akakhala ndi chilema chilichonse, asayandikire malo opatulika. Kaya akhale wakhungu, wolumala, wamphuno yokhadzuka, wa chiwalo chimodzi chachitali kwambiri kuposa chinzake,+
18 Munthu akakhala ndi chilema chilichonse, asayandikire malo opatulika. Kaya akhale wakhungu, wolumala, wamphuno yokhadzuka, wa chiwalo chimodzi chachitali kwambiri kuposa chinzake,+