Deuteronomo 27:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 “‘Wotembereredwa ndi munthu wobisalira mnzake ndi kumupha.’+ (Anthu onse ayankhe kuti, ‘Zikhale momwemo!’) Salimo 109:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ana ake azingoyendayenda ndithu,+Ndipo azipemphapempha.Azichoka m’mabwinja mmene akukhala, n’kupita kukafunafuna chakudya.+
24 “‘Wotembereredwa ndi munthu wobisalira mnzake ndi kumupha.’+ (Anthu onse ayankhe kuti, ‘Zikhale momwemo!’)
10 Ana ake azingoyendayenda ndithu,+Ndipo azipemphapempha.Azichoka m’mabwinja mmene akukhala, n’kupita kukafunafuna chakudya.+