2 Samueli 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Isi-boseti mwana wa Sauli anali ndi zaka 40 pamene anakhala mfumu ya Isiraeli, ndipo analamulira zaka ziwiri. Anthu a nyumba ya Yuda+ okha ndi amene anali kutsatira Davide.
10 Isi-boseti mwana wa Sauli anali ndi zaka 40 pamene anakhala mfumu ya Isiraeli, ndipo analamulira zaka ziwiri. Anthu a nyumba ya Yuda+ okha ndi amene anali kutsatira Davide.