2 Samueli 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 pamene munthu wina anandibweretsera uthenga+ wakuti, ‘Sauli wafa,’ ndipo iye anali kuganiza kuti wabweretsa uthenga wabwino, ine ndinamugwira ndi kumupha+ ku Zikilaga m’malo momulipira monga mthenga.
10 pamene munthu wina anandibweretsera uthenga+ wakuti, ‘Sauli wafa,’ ndipo iye anali kuganiza kuti wabweretsa uthenga wabwino, ine ndinamugwira ndi kumupha+ ku Zikilaga m’malo momulipira monga mthenga.