2 Samueli 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Rekabu ndi Bana, ana aamuna a Rimoni Mbeeroti, ananyamuka kupita kunyumba ya Isi-boseti+ masana kutatentha, ndipo anamupeza akugona. 1 Mafumu 8:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 inu mumve muli kumwamba ndipo muchitepo kanthu mwa kusonyeza amene ali wolakwa pom’bwezera mogwirizana ndi njira yake,+ ndi kusonyeza amene ali wolungama+ pom’patsa mphoto mogwirizana ndi chilungamo chake.+
5 Rekabu ndi Bana, ana aamuna a Rimoni Mbeeroti, ananyamuka kupita kunyumba ya Isi-boseti+ masana kutatentha, ndipo anamupeza akugona.
32 inu mumve muli kumwamba ndipo muchitepo kanthu mwa kusonyeza amene ali wolakwa pom’bwezera mogwirizana ndi njira yake,+ ndi kusonyeza amene ali wolungama+ pom’patsa mphoto mogwirizana ndi chilungamo chake.+