1 Mbiri 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Patapita nthawi, Aisiraeli+ onse anasonkhana kwa Davide ku Heburoni+ ndi kumuuza kuti: “Ife ndife fupa lanu ndi mnofu wanu.+ 1 Mbiri 12:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Tsopano nazi ziwerengero za atsogoleri a anthu okonzekera kumenya nkhondo amene anabwera kwa Davide ku Heburoni,+ kudzam’patsa ufumu+ wa Sauli malinga ndi lamulo la Yehova.+
11 Patapita nthawi, Aisiraeli+ onse anasonkhana kwa Davide ku Heburoni+ ndi kumuuza kuti: “Ife ndife fupa lanu ndi mnofu wanu.+
23 Tsopano nazi ziwerengero za atsogoleri a anthu okonzekera kumenya nkhondo amene anabwera kwa Davide ku Heburoni,+ kudzam’patsa ufumu+ wa Sauli malinga ndi lamulo la Yehova.+