1 Mbiri 14:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Davide anatenganso akazi ena+ mu Yerusalemu, ndipo anaberekanso ana ena aamuna ndi aakazi.+