1 Mbiri 14:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ku Yerusalemu, Davide anakwatiranso akazi ena+ ndipo anaberekanso ana ena aamuna ndi aakazi.+