2 Samueli 22:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Koma mudzachititsa adani anga kugonja* pamaso panga,+Anthu odana nane kwambiri, ndidzawakhalitsa chete.+ Salimo 29:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 M’patseni Yehova ulemerero woyenera dzina lake.+Weramirani Yehova mutavala zovala zopatulika zokongola.+
41 Koma mudzachititsa adani anga kugonja* pamaso panga,+Anthu odana nane kwambiri, ndidzawakhalitsa chete.+
2 M’patseni Yehova ulemerero woyenera dzina lake.+Weramirani Yehova mutavala zovala zopatulika zokongola.+