1 Mbiri 13:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Atatero, Davide ndi Aisiraeli onse ananyamuka kupita ku Baala,+ ku Kiriyati-yearimu, amene ali m’dera la Yuda. Anapita kumeneko kukatenga likasa la Mulungu woona, Yehova, wokhala pa akerubi.+ Palikasa limeneli, amaitanirapo dzina lake.
6 Atatero, Davide ndi Aisiraeli onse ananyamuka kupita ku Baala,+ ku Kiriyati-yearimu, amene ali m’dera la Yuda. Anapita kumeneko kukatenga likasa la Mulungu woona, Yehova, wokhala pa akerubi.+ Palikasa limeneli, amaitanirapo dzina lake.