Yoswa 15:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kuchokera pamwamba pa phirilo, malirewo anakafika kukasupe wa madzi a Nafitoa,+ n’kupitirira mpaka kumizinda ya m’mphepete mwa phiri la Efuroni. Anapitirirabe mpaka ku Baala,+ kutanthauza Kiriyati-yearimu.+ Yoswa 15:60 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 60 Kiriyati-baala,+ kutanthauza Kiriyati-yearimu,+ ndi Raba. Mizinda iwiri ndi midzi yake.
9 Kuchokera pamwamba pa phirilo, malirewo anakafika kukasupe wa madzi a Nafitoa,+ n’kupitirira mpaka kumizinda ya m’mphepete mwa phiri la Efuroni. Anapitirirabe mpaka ku Baala,+ kutanthauza Kiriyati-yearimu.+