1 Mbiri 13:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pamenepo Davide sanatenge Likasa kupita nalo kumene anali kukhala ku Mzinda wa Davide. M’malomwake, analipatutsira kunyumba ya Obedi-edomu+ Mgiti.+
13 Pamenepo Davide sanatenge Likasa kupita nalo kumene anali kukhala ku Mzinda wa Davide. M’malomwake, analipatutsira kunyumba ya Obedi-edomu+ Mgiti.+