1 Mbiri 13:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Likasa la Mulungu woona linakhalabe ndi banja la Obedi-edomu kunyumba kwake+ kwa miyezi itatu, ndipo Yehova anapitiriza kudalitsa+ banja la Obedi-edomu, ndi zinthu zake zonse.
14 Likasa la Mulungu woona linakhalabe ndi banja la Obedi-edomu kunyumba kwake+ kwa miyezi itatu, ndipo Yehova anapitiriza kudalitsa+ banja la Obedi-edomu, ndi zinthu zake zonse.