2 Samueli 6:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Likasa la Yehova linakhalabe kunyumba ya Obedi-edomu Mgiti kwa miyezi itatu, ndipo Yehova anapitiriza kudalitsa+ Obedi-edomu ndi banja lake lonse.+
11 Likasa la Yehova linakhalabe kunyumba ya Obedi-edomu Mgiti kwa miyezi itatu, ndipo Yehova anapitiriza kudalitsa+ Obedi-edomu ndi banja lake lonse.+