Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 30:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Koma Labani anauza Yakobo kuti: “Ngati wandikomera mtima, ungokhala konkuno. Ndaombeza maula ndipo ndapeza kuti Yehova akundidalitsa chifukwa cha iwe.”+

  • Genesis 39:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Kuyambira pamene Potifara anasankha Yosefe kukhala woyang’anira nyumba yake ndi zinthu zake zonse, Yehova anapitiriza kudalitsa nyumba ya Mwiguputoyo chifukwa cha Yosefe. Yehova anadalitsa zonse za m’nyumba ya Potifara ndi zakumunda zomwe.+

  • Miyambo 10:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Madalitso a Yehova ndi amene amalemeretsa,+ ndipo sawonjezerapo ululu.+

  • Malaki 3:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Bweretsani gawo limodzi mwa magawo 10 alionse a zinthu zanu+ n’kuziika mosungiramo zinthu zanga, kuti m’nyumba mwanga mukhale chakudya.+ Ndiyeseni chonde pa nkhani imeneyi,+ kuti muone ngati sindidzakutsegulirani zipata za kumwamba+ ndi kukukhuthulirani madalitso oti mudzasowa powalandirira,”+ watero Yehova wa makamu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena