Genesis 30:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma Labani anauza Yakobo kuti: “Ngati wandikomera mtima, ungokhala konkuno. Ndaombeza maula ndipo ndapeza kuti Yehova akundidalitsa chifukwa cha iwe.”+ Deuteronomo 28:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Udzakhala wodalitsika mumzinda,+ udzakhala wodalitsika m’munda.+ 2 Samueli 6:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Likasa la Yehova linakhalabe kunyumba ya Obedi-edomu Mgiti kwa miyezi itatu, ndipo Yehova anapitiriza kudalitsa+ Obedi-edomu ndi banja lake lonse.+
27 Koma Labani anauza Yakobo kuti: “Ngati wandikomera mtima, ungokhala konkuno. Ndaombeza maula ndipo ndapeza kuti Yehova akundidalitsa chifukwa cha iwe.”+
11 Likasa la Yehova linakhalabe kunyumba ya Obedi-edomu Mgiti kwa miyezi itatu, ndipo Yehova anapitiriza kudalitsa+ Obedi-edomu ndi banja lake lonse.+