Yoswa 18:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako khamu lonse la ana a Isiraeli linasonkhana ku Silo,+ ndipo kumeneko anamangako chihema chokumanako,+ popeza anali atagonjetsa dziko lomwe linali pamaso pawo.+ 1 Mafumu 8:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 ‘Kuchokera tsiku limene ndinatulutsa anthu anga Aisiraeli m’dziko la Iguputo, sindinasankhe+ mzinda m’mafuko onse a Isiraeli woti iwo amangeko nyumba+ ya dzina langa+ kuti likhale kumeneko. Koma ndidzasankha Davide kuti alamulire anthu anga Aisiraeli.’+
18 Kenako khamu lonse la ana a Isiraeli linasonkhana ku Silo,+ ndipo kumeneko anamangako chihema chokumanako,+ popeza anali atagonjetsa dziko lomwe linali pamaso pawo.+
16 ‘Kuchokera tsiku limene ndinatulutsa anthu anga Aisiraeli m’dziko la Iguputo, sindinasankhe+ mzinda m’mafuko onse a Isiraeli woti iwo amangeko nyumba+ ya dzina langa+ kuti likhale kumeneko. Koma ndidzasankha Davide kuti alamulire anthu anga Aisiraeli.’+