Deuteronomo 9:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pamenepo ndinayamba kupembedzera+ Yehova ndi kunena kuti, ‘Yehova Ambuye Wamkulu Koposa, musawononge anthu anu, amene ndiwo chuma chanu chapadera,+ anthu amene munawawombola ndi mphamvu yanu, amene munawatulutsa mu Iguputo+ ndi dzanja lamphamvu.+ Nehemiya 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iwo ndi atumiki anu+ ndi anthu anu,+ amene munawawombola ndi mphamvu zanu zazikulu+ ndi dzanja lanu lamphamvu.+
26 Pamenepo ndinayamba kupembedzera+ Yehova ndi kunena kuti, ‘Yehova Ambuye Wamkulu Koposa, musawononge anthu anu, amene ndiwo chuma chanu chapadera,+ anthu amene munawawombola ndi mphamvu yanu, amene munawatulutsa mu Iguputo+ ndi dzanja lamphamvu.+
10 Iwo ndi atumiki anu+ ndi anthu anu,+ amene munawawombola ndi mphamvu zanu zazikulu+ ndi dzanja lanu lamphamvu.+