Deuteronomo 26:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndipo lero Yehova wakuchititsani kunena kuti mudzakhala anthu ake, chuma chapadera,+ monga mmene anakulonjezerani,+ ndiponso kuti mudzasunga malamulo ake onse, 1 Mbiri 17:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Inutu munapanga anthu anu Aisiraeli kuti akhaledi anthu anu+ mpaka kalekale. Ndipo inu Yehova munakhala Mulungu wawo.+
18 Ndipo lero Yehova wakuchititsani kunena kuti mudzakhala anthu ake, chuma chapadera,+ monga mmene anakulonjezerani,+ ndiponso kuti mudzasunga malamulo ake onse,
22 Inutu munapanga anthu anu Aisiraeli kuti akhaledi anthu anu+ mpaka kalekale. Ndipo inu Yehova munakhala Mulungu wawo.+