1 Mbiri 18:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pamene Asiriya a ku Damasiko anabwera kudzathandiza Hadadezeri mfumu ya Zoba,+ Davide anapha amuna 22,000 a ku Siriya.
5 Pamene Asiriya a ku Damasiko anabwera kudzathandiza Hadadezeri mfumu ya Zoba,+ Davide anapha amuna 22,000 a ku Siriya.