1 Mbiri 18:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Komanso Davide anatenga mkuwa wambirimbiri ku Tibati+ ndi ku Kuni, mizinda ya Hadadezeri. Solomo anagwiritsa ntchito mkuwa umenewu kupangira thanki lamkuwa,+ zipilala+ ndi ziwiya zamkuwa.+
8 Komanso Davide anatenga mkuwa wambirimbiri ku Tibati+ ndi ku Kuni, mizinda ya Hadadezeri. Solomo anagwiritsa ntchito mkuwa umenewu kupangira thanki lamkuwa,+ zipilala+ ndi ziwiya zamkuwa.+