-
1 Mbiri 18:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 nthawi yomweyo anatumiza mwana wake Hadoramu+ kwa Mfumu Davide kukamufunsa za moyo wake ndi kumuyamikira chifukwa chomenyana ndi Hadadezeri ndi kumugonjetsa (pakuti Hadadezeri ndi Tou anali kumenyana kawirikawiri). Popita kwa Davide, Hadoramu anatenga zinthu zosiyanasiyana zagolide, zasiliva,+ ndi zamkuwa.
-