Yobu 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Aliyense wosasonyeza mnzake kukoma mtima kosatha,+Adzasiyanso kuopa Wamphamvuyonse.+ Miyambo 11:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Munthu wosonyeza kukoma mtima kosatha amapindulitsa moyo wake,+ koma munthu wankhanza amachititsa kuti thupi lake linyanyalidwe.+
17 Munthu wosonyeza kukoma mtima kosatha amapindulitsa moyo wake,+ koma munthu wankhanza amachititsa kuti thupi lake linyanyalidwe.+