2 Samueli 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno Davide ananena kuti: “Kodi pali aliyense wotsala wa m’nyumba ya Sauli? Ndikufuna kumusonyeza kukoma mtima kosatha+ chifukwa cha Yonatani.”+
9 Ndiyeno Davide ananena kuti: “Kodi pali aliyense wotsala wa m’nyumba ya Sauli? Ndikufuna kumusonyeza kukoma mtima kosatha+ chifukwa cha Yonatani.”+