2 Samueli 19:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Iye anali ndi amuna 1,000 ochokera ku Benjamini. (Analinso ndi Ziba+ mtumiki wa nyumba ya Sauli pamodzi ndi ana ake 15+ ndi atumiki ake 20. Iwo anakwanitsa kukafika ku Yorodano mfumu isanafike.
17 Iye anali ndi amuna 1,000 ochokera ku Benjamini. (Analinso ndi Ziba+ mtumiki wa nyumba ya Sauli pamodzi ndi ana ake 15+ ndi atumiki ake 20. Iwo anakwanitsa kukafika ku Yorodano mfumu isanafike.