Genesis 24:53 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 Kenako, mtumikiyo anayamba kutulutsa zinthu zasiliva, zagolide, ndi zovala n’kupatsa Rabeka. Anaperekanso zinthu zamtengo wapatali kwa mlongo wake wa Rabeka ndi kwa mayi ake.+
53 Kenako, mtumikiyo anayamba kutulutsa zinthu zasiliva, zagolide, ndi zovala n’kupatsa Rabeka. Anaperekanso zinthu zamtengo wapatali kwa mlongo wake wa Rabeka ndi kwa mayi ake.+