-
1 Mbiri 19:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Zitachitika zimenezi, Davide anati: “Ndidzasonyeza Hanuni mwana wa Nahasi kukoma mtima kosatha,+ chifukwa bambo ake anandisonyeza kukoma mtima kosatha.”+ Chotero Davide anatumiza amithenga kuti akatonthoze Hanuni chifukwa cha imfa ya bambo ake, ndipo atumiki a Davidewo anafika m’dziko la ana a Amoni+ kwa Hanuni kuti amutonthoze.
-