Yobu 24:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Diso la wachigololo+ limadikira kuti mdima ugwe madzulo.+Iye amati, ‘Palibe diso limene lindione,’+Ndipo amaphimba kumaso kwake. Yohane 3:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Amene amachita zinthu zoipa+ amadana ndi kuwala ndipo safika pamene pali kuwala, kuti ntchito zake zisadzudzulidwe.+
15 Diso la wachigololo+ limadikira kuti mdima ugwe madzulo.+Iye amati, ‘Palibe diso limene lindione,’+Ndipo amaphimba kumaso kwake.
20 Amene amachita zinthu zoipa+ amadana ndi kuwala ndipo safika pamene pali kuwala, kuti ntchito zake zisadzudzulidwe.+