Genesis 39:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pamenepo mkaziyo anam’gwira malaya+ mnyamatayo n’kumuuza kuti: “Ugone nane basi!”+ Koma mnyamatayo anangovula malayawo n’kuwasiya m’manja mwa mkaziyo n’kuthawira panja.+
12 Pamenepo mkaziyo anam’gwira malaya+ mnyamatayo n’kumuuza kuti: “Ugone nane basi!”+ Koma mnyamatayo anangovula malayawo n’kuwasiya m’manja mwa mkaziyo n’kuthawira panja.+