Genesis 39:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako, mkazi wa mbuyake anayamba kuyang’ana Yosefe momusirira,+ moti anali kumuuza kuti: “Ugone nane.”+
7 Kenako, mkazi wa mbuyake anayamba kuyang’ana Yosefe momusirira,+ moti anali kumuuza kuti: “Ugone nane.”+