Genesis 37:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Isiraeli anali kum’konda kwambiri Yosefe kuposa ana ake ena onse,+ chifukwa anali mwana amene anam’bereka atakalamba. Chotero anam’soketsera mkanjo wamizeremizere wamanja aatali.+
3 Isiraeli anali kum’konda kwambiri Yosefe kuposa ana ake ena onse,+ chifukwa anali mwana amene anam’bereka atakalamba. Chotero anam’soketsera mkanjo wamizeremizere wamanja aatali.+