Rute 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako Boazi anafika kuchokera ku Betelehemu ndipo anauza okololawo kuti: “Yehova akhale nanu.”+ Iwo anayankha mwa nthawi zonse kuti: “Yehova akudalitseni.”+
4 Kenako Boazi anafika kuchokera ku Betelehemu ndipo anauza okololawo kuti: “Yehova akhale nanu.”+ Iwo anayankha mwa nthawi zonse kuti: “Yehova akudalitseni.”+