1 Mafumu 21:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Choncho amuna a mumzinda wake, akulu ndi anthu olemekezeka amene anali kukhala mumzindawo, anachita zimene Yezebeli anawatuma, mogwirizana ndi zimene iye analemba m’makalata amene anawatumizira.+
11 Choncho amuna a mumzinda wake, akulu ndi anthu olemekezeka amene anali kukhala mumzindawo, anachita zimene Yezebeli anawatuma, mogwirizana ndi zimene iye analemba m’makalata amene anawatumizira.+