2 Samueli 13:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Chotero Abisalomu anathawa ndi kupita ku Gesuri+ ndipo anakhala kumeneko zaka zitatu. 2 Samueli 14:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Yowabu atanena mawu amenewa ananyamuka ndi kupita ku Gesuri,+ ndipo anabweretsa Abisalomu ku Yerusalemu.+
23 Yowabu atanena mawu amenewa ananyamuka ndi kupita ku Gesuri,+ ndipo anabweretsa Abisalomu ku Yerusalemu.+