Salimo 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Inu Yehova, n’chifukwa chiyani adani anga achuluka chotere?+N’chifukwa chiyani anthu ondiukira achuluka?+ Salimo 43:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Ndiweruzeni+ inu Mulungu,Weruzani mlandu wanga+ motsutsana ndi mtundu wosakhulupirika.Ndipulumutseni kwa munthu wachinyengo ndi wochita zosalungama.+ Miyambo 24:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mwana wanga uziopa Yehova ndiponso mfumu.+ Usamakhale pagulu la anthu ofuna kuti zinthu zisinthe,+
3 Inu Yehova, n’chifukwa chiyani adani anga achuluka chotere?+N’chifukwa chiyani anthu ondiukira achuluka?+
43 Ndiweruzeni+ inu Mulungu,Weruzani mlandu wanga+ motsutsana ndi mtundu wosakhulupirika.Ndipulumutseni kwa munthu wachinyengo ndi wochita zosalungama.+
21 Mwana wanga uziopa Yehova ndiponso mfumu.+ Usamakhale pagulu la anthu ofuna kuti zinthu zisinthe,+