Miyambo 18:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pali mabwenzi amene amafuna kuthyolana,+ koma pali bwenzi limene limamatirira kuposa m’bale wako.+ Luka 22:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 “Komabe, inu mwakhalabe ndi ine+ m’mayesero anga.+ Yohane 15:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mupitiriza kukhala mabwenzi anga mukamachita zimene ndikukulamulani.+ 1 Akorinto 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Komanso pamenepa, chofunika kwa woyang’anira+ ndicho kukhala wokhulupirika.+
24 Pali mabwenzi amene amafuna kuthyolana,+ koma pali bwenzi limene limamatirira kuposa m’bale wako.+